Depository of News

Bokosi si chitukuko

newsdepo.com · world

Mafumu ena m’dziko muno apempha aphungu a ku Nyumba ya Malamulo kuti asiye kugula mabokosi pa maliro ponena kuti bokosi la maliro si chitukuko. Mafumuwa ati izi zikulimbikitsa kuti anthu azikhala akudalira kalikonse kuchoka kwa aphungu zomwe zimachititsa kuti aphunguwo asiye kulunjika pa nsanja zokweza dziko lino ku nkhani ya chitukuko. Malingana ndi a Gulupu … The post Bokosi si chitukuko appeared first on Nation Online .

Read full article →