Umboni wa ngozi uvuta
Komiti yomwe ikufufuza ngozi ya ndege yomwe adali wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima ndi anthu ena 8 pa 10 June 2024 yamva umboni osiyanasiyana koma mkati mwa sabatayi mwatuluka umboni wogonthetsa m’makutu kuchokera kwa mboni zomwe zikuti zidali pa malo a ngoziyo ikuchitika. Lachinayi, membala wachitetezo cha m’mudzi ku dera lomwe … The post Umboni wa ngozi uvuta appeared first on Nation Online .
