Akufuna kumanga nyumba zoteteza ofuna kudzipha
<p>Bungwe la Azibambo Tibe Khonde Mental Health Initiative lati likufuna kukhala ndi malo 14 m’dziko la Malawi kumene anthu angakatule nkhawa zawo pomwe malingaliro odzipha akuyala nthenje m’mitu yawo. Mkulu wa bungwelo a Jefferson Milanzi ndiwo anena izi lero pamene dziko la Malawi lili limodzi ndi maiko onse a dziko la pansi polingalira zokumbutsa kuti …</p> <p>The post <a href="https://mwnation.com/akufuna-kumanga-nyumba-zoteteza-ofuna-kudzipha/">Akufuna kumanga nyumba zoteteza ofuna kudzipha</a> appeared first on <a href="https://mwnation.com">Nation Online</a>.</p>
