Depository of News

A Mtsiro aiphula

newsdepo.com · tech

<p>Maumboni oyamikira a Ledson Mtsiro akuyenda ngati madzi m’masamba a mchezo pamene Amalawi 423 adasonkha pafupifupi K6.1 miliyoni powathokoza pa ntchito ya chitetezo imene amagwira Pa Game mu mzinda wa Lilongwe. Ndipo anthu ena a kufuna kwabwino awapatsa a Mtsiro mapuloti awiri ndipo gawo lina la ndalamazo agulira njinga ya moto komanso laputopu ya mwana &#8230;</p> <p>The post <a href="https://mwnation.com/a-mtsiro-aiphula/">A Mtsiro aiphula</a> appeared first on <a href="https://mwnation.com">Nation Online</a>.</p>

Read full article →