Depository of News

Mkokemkoke pa za maufumu

newsdepo.com · world

<p>Pali mkokemkoke pakati pa maufumu a m’dziko lino ndi boma pa malire amene mbali ziwirizi zingatenge potsatira malamulo. Chikalata chimene adasaina mlembi wamkulu wa unduna woona za maboma aang’ono mbusa Moses Chimphepo adalemba pa 7 September. Iwo adati malamulo salola kuti m’dziko muno mukhale maufumu, kingdom m’Chingerezi, ndipo pasakhale wina wotchedwa mfumu ya mtundu. M’mbelwa &#8230;</p> <p>The post <a href="https://mwnation.com/mkokemkoke-pa-za-maufumu/">Mkokemkoke pa za maufumu</a> appeared first on <a href="https://mwnation.com">Nation Online</a>.</p>

Read full article →