Amalizitsa ntchito yosamutsa Amalawi ku Joni
<p>Gulu lomwe lakhala likuthandiza anthu omwe adathawa m’nyumba zawo ndipo amakhala movutika kutsatira zipolowe zothotha anthu a maiko ena m’dziko la South Africa (SA) lati latsiriza ntchitoyo. Mwa zina, gululi lakhala likupereka thandizo monga chakudya komanso mayendedwe kwa anthuwa kwa miyezi inayi. Gulu lomaliza la anthu 43 lidafika m’dziko muno usiku wa dzulo Lachitatu kuchokera …</p> <p>The post <a href="https://mwnation.com/amalizitsa-ntchito-yosamutsa-amalawi-ku-joni/">Amalizitsa ntchito yosamutsa Amalawi ku Joni</a> appeared first on <a href="https://mwnation.com">Nation Online</a>.</p>
