Akusaka wopha malume chifukwa cha mtengo
Apolisi ku Chiradzulu akufunafuna bambo wa zaka 35 a Michael Mkandawire, powaganizira kuti adamenya malume ake a zaka 65, a Rodrick Michael, mpaka kufa pa mkangano wokhudza mtengo wa mango. Izi zidachitika pa 24 October 2026 m’mudzi wa Nanyanga, m’dera la T/A Likoswe, malinga ndi wachiwiri kwa mneneri wa polisi ku Chiradzulu a Andrew Kusimbwa. … The post Akusaka wopha malume chifukwa cha mtengo appeared first on Nation Online .
