Depository of News

Mikunzi ya DPP yaombana mitu

newsdepo.com · world

Mikunzi iwiri ya Democratic Progressive Party (DPP) yautsirana chenjelere pa nkhani ya ziphuphu m’boma. A Sipikala a Nyumba ya Malamulo a Sameer Suleman adauza Asilamu pa mzikiti wa ku Area 13 ku Lilongwe kuti ziphuphu zidamanga nthenje m’boma moti n’kovuta kuti atsogoleri athane nazo. A Suleman akufuna kuchepetsa ziphuphu. I Nation A Suleman, omwe ndi … The post Mikunzi ya DPP yaombana mitu appeared first on Nation Online .

Read full article →