Lamulo la za umoyo likulephera kuluma
Lamulo la za umoyo la m’chaka cha 2019 likulephera kugwira ntchito kaamba koti lilibe mndondomeko. Cholinga cha lamuloli chidali kukhwimitsa ntchito zaumoyo poteteza mankhwala, kuchepetsa mchitidwe wogulitsa mankhwala osayenera ku boma, komanso kuletsa mankhwala osavomerezeka azitsamba. Staff shortages have resulted in one worker serving 1 495 people. | Nation Mkulu wa bungwe la Malawi Health … The post Lamulo la za umoyo likulephera kuluma appeared first on Nation Online .
